1 Samueli 25:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Iwenso udalitsike chifukwa cha kuganiza bwino kwako. Udalitsike chifukwa chondiletsa kuti ndisapalamule mlandu wa magazi+ ndiponso kuti ndisabwezere* ndekha ndi manja anga.
33 Iwenso udalitsike chifukwa cha kuganiza bwino kwako. Udalitsike chifukwa chondiletsa kuti ndisapalamule mlandu wa magazi+ ndiponso kuti ndisabwezere* ndekha ndi manja anga.