1 Samueli 25:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo wa Isiraeli, amene wandiletsa kuti ndisakuchitire zoipa,+ ukanapanda kubwera mwamsanga kudzakumana ndi ine,+ ndithu sipakanatsala mwamuna* aliyense wamʼbanja la Nabala pofika mawa mʼmawa.”+
34 Mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo wa Isiraeli, amene wandiletsa kuti ndisakuchitire zoipa,+ ukanapanda kubwera mwamsanga kudzakumana ndi ine,+ ndithu sipakanatsala mwamuna* aliyense wamʼbanja la Nabala pofika mawa mʼmawa.”+