1 Samueli 25:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Abigayeli anapita kwa Nabala ndipo anamupeza mʼnyumba mwake akuchita phwando ngati la mfumu. Nabala* anali akusangalala kwambiri ndiponso ataledzereratu. Abigayeli sanamuuze chilichonse mpaka mʼmawa. 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:36 Tsanzirani, ptsa. 80-82 Nsanja ya Olonda,7/1/2009, tsa. 21
36 Abigayeli anapita kwa Nabala ndipo anamupeza mʼnyumba mwake akuchita phwando ngati la mfumu. Nabala* anali akusangalala kwambiri ndiponso ataledzereratu. Abigayeli sanamuuze chilichonse mpaka mʼmawa.