-
1 Samueli 25:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Mʼmawa kutacha, vinyo atamuthera mʼmutu, mkazi wake anamuuza zonse zimene zinachitika. Nabala atamva zimenezi, mtima wake unaferatu ndipo anauma ngati mwala.
-