-
1 Samueli 25:40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 Choncho atumiki a Davide anapita kwa Abigayeli ku Karimeli ndipo anamuuza kuti: “Davide watituma kuti tidzakutenge ukakhale mkazi wake.”
-