1 Samueli 25:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Nthawi yomweyo, ananyamuka nʼkugwada mpaka nkhope yake kufika pansi, ndipo ananena kuti: “Ine kapolo wanu ndine wokonzeka kukhala wantchito wosambitsa mapazi+ a atumiki a mbuyanga.” 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:41 Tsanzirani, ptsa. 82-83 Nsanja ya Olonda,7/1/2009, tsa. 21
41 Nthawi yomweyo, ananyamuka nʼkugwada mpaka nkhope yake kufika pansi, ndipo ananena kuti: “Ine kapolo wanu ndine wokonzeka kukhala wantchito wosambitsa mapazi+ a atumiki a mbuyanga.”