1 Samueli 25:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Kenako Abigayeli+ ananyamuka mofulumira nʼkukwera pabulu ndipo atsikana ake 5 antchito ankamutsatira pambuyo. Iye anapita limodzi ndi anthu amene anatumidwa ndi Davide ndipo anakakhala mkazi wake. 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:42 Tsanzirani, ptsa. 82-83 Nsanja ya Olonda,7/1/2009, tsa. 21
42 Kenako Abigayeli+ ananyamuka mofulumira nʼkukwera pabulu ndipo atsikana ake 5 antchito ankamutsatira pambuyo. Iye anapita limodzi ndi anthu amene anatumidwa ndi Davide ndipo anakakhala mkazi wake.