1 Samueli 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Patapita nthawi, amuna a ku Zifi+ anapita kwa Sauli ku Gibeya+ kukamuuza kuti: “Davide akubisala kuphiri la Hakila mbali imene yayangʼanizana ndi Yesimoni.”*+
26 Patapita nthawi, amuna a ku Zifi+ anapita kwa Sauli ku Gibeya+ kukamuuza kuti: “Davide akubisala kuphiri la Hakila mbali imene yayangʼanizana ndi Yesimoni.”*+