1 Samueli 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako Davide anapita kumene Sauli anamanga msasa. Iye anaona pamene Sauli komanso Abineri+ mwana wa Nera, mtsogoleri wa asilikali, anagona. Sauli anali atagona pakati pa msasa ndipo asilikali onse anagona momuzungulira.
5 Kenako Davide anapita kumene Sauli anamanga msasa. Iye anaona pamene Sauli komanso Abineri+ mwana wa Nera, mtsogoleri wa asilikali, anagona. Sauli anali atagona pakati pa msasa ndipo asilikali onse anagona momuzungulira.