1 Samueli 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Davide anauza Ahimeleki Muhiti+ ndi Abisai+ mwana wa Zeruya,+ mchimwene wake wa Yowabu, kuti: “Ndani apite nane kwa Sauli kumsasa?” Abisai anayankha kuti: “Ine ndipita nanu.”
6 Ndiyeno Davide anauza Ahimeleki Muhiti+ ndi Abisai+ mwana wa Zeruya,+ mchimwene wake wa Yowabu, kuti: “Ndani apite nane kwa Sauli kumsasa?” Abisai anayankha kuti: “Ine ndipita nanu.”