1 Samueli 26:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Davide anapitiriza kuti: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova, Mulungu wamoyo, Yehova adzamulanga yekha,+ kapena tsiku lidzafika+ ndipo adzamwalira, kapenanso adzapita kunkhondo nʼkukaphedwa.+
10 Davide anapitiriza kuti: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova, Mulungu wamoyo, Yehova adzamulanga yekha,+ kapena tsiku lidzafika+ ndipo adzamwalira, kapenanso adzapita kunkhondo nʼkukaphedwa.+