1 Samueli 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho Davide anatenga mkondo ndi jagi ya madzi zimene zinali chakumutu kwa Sauli nʼkumapita. Palibe aliyense amene anadzuka, kuwaona+ kapena kuzindikira, chifukwa onse anali mʼtulo tofa nato tochokera kwa Yehova.
12 Choncho Davide anatenga mkondo ndi jagi ya madzi zimene zinali chakumutu kwa Sauli nʼkumapita. Palibe aliyense amene anadzuka, kuwaona+ kapena kuzindikira, chifukwa onse anali mʼtulo tofa nato tochokera kwa Yehova.