-
1 Samueli 26:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Mbuyanga mfumu, mvetserani mawu anga, ine mtumiki wanu: Ngati Yehova ndi amene wakutumani kuti mulimbane nane, iye alandire* nsembe yanga yambewu. Koma ngati ndi anthu amene akutumani,+ atembereredwe pamaso pa Yehova, chifukwa andithamangitsa lero kuti ndisakhale pamalo omwe ndi cholowa cha Yehova+ ndipo andiuza kuti, ‘Pita ukatumikire milungu ina!’
-