1 Samueli 26:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Musalole kuti magazi anga akhetsedwe pamaso pa Yehova, chifukwa mfumu ya Isiraeli yapita kukasakasaka nthata imodzi+ ngati ikuthamangitsa nkhwali imodzi mʼmapiri.”
20 Musalole kuti magazi anga akhetsedwe pamaso pa Yehova, chifukwa mfumu ya Isiraeli yapita kukasakasaka nthata imodzi+ ngati ikuthamangitsa nkhwali imodzi mʼmapiri.”