1 Samueli 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Sauli anayankha kuti: “Ndachimwa.+ Bwerera mwana wanga Davide. Sindidzakusakasakanso chifukwa lero waona kuti moyo wanga ndi wamtengo wapatali.+ Ndachita zinthu mopusa komanso ndalakwitsa kwambiri.”
21 Sauli anayankha kuti: “Ndachimwa.+ Bwerera mwana wanga Davide. Sindidzakusakasakanso chifukwa lero waona kuti moyo wanga ndi wamtengo wapatali.+ Ndachita zinthu mopusa komanso ndalakwitsa kwambiri.”