1 Samueli 26:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova ndi amene adzabwezera aliyense mogwirizana ndi chilungamo chake+ komanso kukhulupirika kwake. Lero Yehova anakuperekani mʼmanja mwanga, koma sindinafune kuvulaza wodzozedwa wa Yehova.+
23 Yehova ndi amene adzabwezera aliyense mogwirizana ndi chilungamo chake+ komanso kukhulupirika kwake. Lero Yehova anakuperekani mʼmanja mwanga, koma sindinafune kuvulaza wodzozedwa wa Yehova.+