1 Samueli 26:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno Sauli anayankha Davide kuti: “Mulungu akudalitse mwana wanga Davide. Mosakayikira iwe udzachita ntchito zazikulu komanso zidzakuyendera bwino.”+ Zitatero, Davide anachoka ndipo Sauli anabwerera kwawo.+
25 Ndiyeno Sauli anayankha Davide kuti: “Mulungu akudalitse mwana wanga Davide. Mosakayikira iwe udzachita ntchito zazikulu komanso zidzakuyendera bwino.”+ Zitatero, Davide anachoka ndipo Sauli anabwerera kwawo.+