1 Samueli 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Davide ankakhala ndi Akisi ku Gati pamodzi ndi amuna amene ankayenda naye, ndipo aliyense anali ndi banja lake. Davide anali ndi akazi awiri, Ahinowamu+ wa ku Yezereeli ndi Abigayeli+ wa ku Karimeli, amene anali mkazi wa Nabala.
3 Davide ankakhala ndi Akisi ku Gati pamodzi ndi amuna amene ankayenda naye, ndipo aliyense anali ndi banja lake. Davide anali ndi akazi awiri, Ahinowamu+ wa ku Yezereeli ndi Abigayeli+ wa ku Karimeli, amene anali mkazi wa Nabala.