1 Samueli 27:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Akisi akafunsa kuti: “Kodi lero munakamenya kuti nkhondo?” Davide ankayankha kuti: “Kumʼmwera kwa dziko* la Yuda”+ kapena “Kumʼmwera kwa dziko la Ayerameeli”+ kapena “Kumʼmwera kwa dziko la Akeni.”+
10 Akisi akafunsa kuti: “Kodi lero munakamenya kuti nkhondo?” Davide ankayankha kuti: “Kumʼmwera kwa dziko* la Yuda”+ kapena “Kumʼmwera kwa dziko la Ayerameeli”+ kapena “Kumʼmwera kwa dziko la Akeni.”+