1 Samueli 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 M‘masiku amenewo Afilisiti anasonkhanitsa asilikali awo kuti akamenyane ndi Aisiraeli.+ Choncho Akisi anauza Davide kuti: “Ukudziwa kuti iwe ndi anthu ako muyenera kupita nane kunkhondo.”+
28 M‘masiku amenewo Afilisiti anasonkhanitsa asilikali awo kuti akamenyane ndi Aisiraeli.+ Choncho Akisi anauza Davide kuti: “Ukudziwa kuti iwe ndi anthu ako muyenera kupita nane kunkhondo.”+