1 Samueli 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Davide anauza Akisi kuti: “Inunso mukudziwa zimene mtumiki wanu angachite.” Atatero Akisi anauza Davide kuti: “Nʼchifukwa chake ndidzakuika kukhala msilikali wondilondera nthawi zonse.”+
2 Davide anauza Akisi kuti: “Inunso mukudziwa zimene mtumiki wanu angachite.” Atatero Akisi anauza Davide kuti: “Nʼchifukwa chake ndidzakuika kukhala msilikali wondilondera nthawi zonse.”+