1 Samueli 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pa nthawiyi nʼkuti Samueli atamwalira ndipo Aisiraeli anali atalira maliro ake nʼkumuika mʼmanda mumzinda wakwawo wa Rama.+ Komanso Sauli anali atachotsa mʼdzikolo anthu olankhula ndi mizimu ndiponso olosera zamʼtsogolo.+
3 Pa nthawiyi nʼkuti Samueli atamwalira ndipo Aisiraeli anali atalira maliro ake nʼkumuika mʼmanda mumzinda wakwawo wa Rama.+ Komanso Sauli anali atachotsa mʼdzikolo anthu olankhula ndi mizimu ndiponso olosera zamʼtsogolo.+