1 Samueli 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Afilisiti anasonkhana nʼkukamanga msasa ku Sunemu.+ Nayenso Sauli anasonkhanitsa Aisiraeli onse nʼkukamanga msasa ku Giliboa.+
4 Afilisiti anasonkhana nʼkukamanga msasa ku Sunemu.+ Nayenso Sauli anasonkhanitsa Aisiraeli onse nʼkukamanga msasa ku Giliboa.+