1 Samueli 28:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Sauli anadzisintha nʼkuvala zovala zina. Atatero, iye ndi anthu awiri anapita kwa mzimayiyo usiku. Ndiyeno Sauliyo anati: “Ndiuze zamʼtsogolo polankhula ndi mizimu+ komanso pondidzutsira munthu amene ndikuuze.”
8 Choncho Sauli anadzisintha nʼkuvala zovala zina. Atatero, iye ndi anthu awiri anapita kwa mzimayiyo usiku. Ndiyeno Sauliyo anati: “Ndiuze zamʼtsogolo polankhula ndi mizimu+ komanso pondidzutsira munthu amene ndikuuze.”