1 Samueli 28:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mzimayiyo ataona “Samueli”*+ anayamba kulira mofuula kwambiri. Kenako anauza Sauli kuti: “Nʼchifukwa chiyani mwandipusitsa? Si inu a Sauli inu?”
12 Mzimayiyo ataona “Samueli”*+ anayamba kulira mofuula kwambiri. Kenako anauza Sauli kuti: “Nʼchifukwa chiyani mwandipusitsa? Si inu a Sauli inu?”