-
1 Samueli 28:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Kenako “Samueli” anafunsa Sauli kuti: “Nʼchifukwa chiyani wandisokoneza pondidzutsa?” Sauli anayankha kuti: “Zinthu zandivuta kwambiri. Afilisiti akumenyana nane koma Mulungu wandisiya ndipo sakundiyankhanso kudzera mwa aneneri kapena mʼmaloto.+ Nʼchifukwa chake ndabwera kwa inu kuti mundiuze zoyenera kuchita.”+
-