1 Samueli 28:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova achita zimene ananena kudzera mwa ine, ndipo Yehova angʼamba ufumu kuuchotsa mʼmanja mwako nʼkuupereka kwa munthu wina, yemwe ndi Davide.+
17 Yehova achita zimene ananena kudzera mwa ine, ndipo Yehova angʼamba ufumu kuuchotsa mʼmanja mwako nʼkuupereka kwa munthu wina, yemwe ndi Davide.+