1 Samueli 28:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Komanso Yehova apereka Aisiraeli ndi iweyo mʼmanja mwa Afilisiti,+ ndipo mawa iwe+ ndi ana ako+ mukhala ndi ine. Yehova aperekanso asilikali a Isiraeli mʼmanja mwa Afilisiti.”+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:19 Nsanja ya Olonda,1/15/1988, ptsa. 3-4
19 Komanso Yehova apereka Aisiraeli ndi iweyo mʼmanja mwa Afilisiti,+ ndipo mawa iwe+ ndi ana ako+ mukhala ndi ine. Yehova aperekanso asilikali a Isiraeli mʼmanja mwa Afilisiti.”+