1 Samueli 28:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mzimayi uja atapita pamene panali Sauli nʼkuona kuti wasokonezeka kwambiri, anamuuza kuti: “Ine mtumiki wanu ndamvera mawu anu ndipo ndaika moyo wanga pangozi+ nʼkuchita zomwe munandiuza.
21 Mzimayi uja atapita pamene panali Sauli nʼkuona kuti wasokonezeka kwambiri, anamuuza kuti: “Ine mtumiki wanu ndamvera mawu anu ndipo ndaika moyo wanga pangozi+ nʼkuchita zomwe munandiuza.