1 Samueli 28:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Atatero anapereka chakudyacho kwa Sauli ndi atumiki ake ndipo iwo anadya. Atamaliza ananyamuka nʼkumapita usiku womwewo.+
25 Atatero anapereka chakudyacho kwa Sauli ndi atumiki ake ndipo iwo anadya. Atamaliza ananyamuka nʼkumapita usiku womwewo.+