1 Samueli 29:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Olamulira a Afilisiti ankadutsa ndi magulu awo a asilikali 100 ndi 1,000, ndipo Davide ndi amuna amene ankayenda naye ankabwera pambuyo pawo limodzi ndi Akisi.+
2 Olamulira a Afilisiti ankadutsa ndi magulu awo a asilikali 100 ndi 1,000, ndipo Davide ndi amuna amene ankayenda naye ankabwera pambuyo pawo limodzi ndi Akisi.+