-
1 Samueli 29:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ndiyeno akalonga a Afilisiti anafunsa kuti: “Kodi Aheberiwa akudzatani kuno?” Akisi anayankha akalonga a Afilisitiwo kuti: “Uyu ndi Davide, mtumiki wa Mfumu Sauli ya Isiraeli. Iye wakhala ndi ine kwa chaka chimodzi kapena kuposa.+ Kuyambira tsiku limene anathawira kwa ine mpaka lero, sindinamupeze ndi vuto lililonse.”
-