4 Koma akalonga a Afilisiti anamʼpsera mtima kwambiri Akisi ndipo anati: “Muuzeni abwerere,+ apite kumalo amene munamʼpatsa. Musamulole kuti apite nafe kunkhondo chifukwa akhoza kukatitembenukira.+ Mukuganiza kuti munthu ameneyu angachite chiyani kuti mbuye wake amukonde? Akaphatu asilikali athu.