1 Samueli 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho Davide anadzuka mʼmamawa pamodzi ndi amuna amene ankayenda naye nʼkubwerera kudziko la Afilisiti. Koma Afilisitiwo anapita ku Yezereeli.+
11 Choncho Davide anadzuka mʼmamawa pamodzi ndi amuna amene ankayenda naye nʼkubwerera kudziko la Afilisiti. Koma Afilisitiwo anapita ku Yezereeli.+