1 Samueli 30:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Davide ndi asilikali ake atafika ku Zikilaga+ tsiku lachitatu, anapeza kuti Aamaleki+ aukira anthu akumʼmwera* ndi amumzinda wa Zikilaga. Iwo anaukira mzindawo nʼkuutentha ndi moto.
30 Davide ndi asilikali ake atafika ku Zikilaga+ tsiku lachitatu, anapeza kuti Aamaleki+ aukira anthu akumʼmwera* ndi amumzinda wa Zikilaga. Iwo anaukira mzindawo nʼkuutentha ndi moto.