1 Samueli 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Davide anayamba kufunsa Yehova+ kuti: “Kodi ndithamangitse gulu la achifwambali? Kodi ndiwapeza?” Iye anamuyankha kuti: “Inde athamangitse chifukwa uwapeza ndithu ndipo ukapulumutsa anthu amene awatenga.”+
8 Ndiyeno Davide anayamba kufunsa Yehova+ kuti: “Kodi ndithamangitse gulu la achifwambali? Kodi ndiwapeza?” Iye anamuyankha kuti: “Inde athamangitse chifukwa uwapeza ndithu ndipo ukapulumutsa anthu amene awatenga.”+