1 Samueli 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nthawi yomweyo, Davide ndi amuna 600+ amene anali naye ananyamuka nʼkuyenda mpaka kukafika kuchigwa cha Besori, ndipo amuna ena anatsala pamenepo.
9 Nthawi yomweyo, Davide ndi amuna 600+ amene anali naye ananyamuka nʼkuyenda mpaka kukafika kuchigwa cha Besori, ndipo amuna ena anatsala pamenepo.