-
1 Samueli 30:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Anamupatsanso keke ya nkhuyu zouma ndi makeke awiri a mphesa zouma. Atadya anapeza mphamvu, chifukwa anakhala osadya chakudya kapena kumwa madzi kwa masiku atatu, masana ndi usiku.
-