1 Samueli 30:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tinakaukira kumʼmwera kwa dziko* la Akereti+ ndi dera la Yuda komanso kumʼmwera kwa dera* la Kalebe.+ Ndipo mzinda wa Zikilaga tinautentha ndi moto.”
14 Tinakaukira kumʼmwera kwa dziko* la Akereti+ ndi dera la Yuda komanso kumʼmwera kwa dera* la Kalebe.+ Ndipo mzinda wa Zikilaga tinautentha ndi moto.”