-
1 Samueli 30:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ndiyeno Davide anamufunsa kuti: “Kodi ungandilondolere kumene kuli gulu la achifwambali?” Iye anayankha kuti: “Ndilumbirireni pamaso pa Mulungu kuti simundipha, komanso kuti simundipereka mʼmanja mwa mbuyanga. Mukatero ndikulondolerani kumene kuli gulu la achifwambali.”
-