-
1 Samueli 30:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Choncho munthuyo analondolera Davide kumene kunali achifwambawo, ndipo anawapeza atamwazikana mʼdziko lonselo, akudya ndi kumwa komanso kusangalala chifukwa chakuti analanda zinthu zambiri mʼdziko la Afilisiti ndi la Yuda.
-