1 Samueli 30:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno Davide anayamba kuwapha kuyambira mʼbandakucha mpaka madzulo. Palibe aliyense amene anapulumuka kupatulapo amuna 400 amene anakwera ngamila nʼkuthawa.+
17 Ndiyeno Davide anayamba kuwapha kuyambira mʼbandakucha mpaka madzulo. Palibe aliyense amene anapulumuka kupatulapo amuna 400 amene anakwera ngamila nʼkuthawa.+