1 Samueli 30:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Davide anatenga zonse zimene Aamaleki analanda+ ndipo anapulumutsanso akazi ake awiri aja.