-
1 Samueli 30:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Choncho Davide anatenga nkhosa zonse ndi ngʼombe zonse za Aamaleki ndipo anthu ake anapita nazo limodzi ndi ziweto zawo. Iwo anati: “Izi ndi zimene Davide walanda.”
-