1 Samueli 30:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako Davide anafika kuchigwa cha Besori kumene kunali amuna 200 omwe anawasiya aja, amene sanathe kupita naye chifukwa anatopa kwambiri.+ Iwo ananyamuka nʼkukalandira Davide ndi anthu amene anali naye. Atakumana, Davide anawafunsa za moyo wawo.
21 Kenako Davide anafika kuchigwa cha Besori kumene kunali amuna 200 omwe anawasiya aja, amene sanathe kupita naye chifukwa anatopa kwambiri.+ Iwo ananyamuka nʼkukalandira Davide ndi anthu amene anali naye. Atakumana, Davide anawafunsa za moyo wawo.