-
1 Samueli 30:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Koma anthu ena oipa ndi opanda pake amene anatsatira Davide anati: “Chifukwa chakuti amenewa sanapite nawo, sitiwapatsa zinthu zimene talandazi. Aliyense tingomupatsa mkazi wake ndi ana ake, kenako azipita.”
-