1 Samueli 30:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndani angavomereze zimenezo? Zomwe alandire munthu amene anapita kunkhondo, zikhala zofanana ndi zimene alandire munthu amene amalondera katundu.+ Aliyense alandirapo kenakake.”+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:24 Nsanja ya Olonda,3/15/2005, tsa. 24
24 Ndani angavomereze zimenezo? Zomwe alandire munthu amene anapita kunkhondo, zikhala zofanana ndi zimene alandire munthu amene amalondera katundu.+ Aliyense alandirapo kenakake.”+