1 Samueli 30:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Davide atafika ku Zikilaga anatumiza zina mwa zinthu zimene analandazo kwa akulu a ku Yuda omwe anali anzake nʼkunena kuti: “Landirani mphatsoyi* kuchokera pa zimene talanda kwa adani a Yehova.”
26 Davide atafika ku Zikilaga anatumiza zina mwa zinthu zimene analandazo kwa akulu a ku Yuda omwe anali anzake nʼkunena kuti: “Landirani mphatsoyi* kuchokera pa zimene talanda kwa adani a Yehova.”