1 Samueli 31:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Afilisiti anayamba kumenyana ndi Aisiraeli+ ndipo asilikali a Isiraeli ankathawa moti ambiri anaphedwa mʼphiri la Giliboa.+
31 Afilisiti anayamba kumenyana ndi Aisiraeli+ ndipo asilikali a Isiraeli ankathawa moti ambiri anaphedwa mʼphiri la Giliboa.+