1 Samueli 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nkhondo inamʼkulira kwambiri Sauli, moti oponya mivi ndi uta anamupeza nʼkumuvulaza koopsa.+